11 Inde inadzikulitsa kufikira kwa kalonga wa khamulo, nimcotsera nsembe yopsereza yacikhalire; ndi pokhala malo ace opatulika panagwetsedwa.
Werengani mutu wathunthu Danieli 8
Onani Danieli 8:11 nkhani