Danieli 9:10 BL92

10 sitinamvera mau a Yehova Mulungu wathu, kuyenda m'malamulo ace anatiikirawo pamaso pathu, mwa atumiki ace aneneri.

Werengani mutu wathunthu Danieli 9

Onani Danieli 9:10 nkhani