Danieli 9:19 BL92

19 Ambu ye, imvani; Ambuye, khululukirani; Ambuye, mverani nimucite; musacedwa, cifukwa ca inu nokha, Mulungu wanga; pakuti mudzi wanu ndi anthu anu anachedwa dzina lanu.

Werengani mutu wathunthu Danieli 9

Onani Danieli 9:19 nkhani