Danieli 9:3 BL92

3 Ndipo ndinaika nkhope yanga kwa Ambuye Mulungu, kumfunsa Iye m'pemphero, ndi mapembedzero, ndi kusala, ndi ziguduli, ndi mapulusa.

Werengani mutu wathunthu Danieli 9

Onani Danieli 9:3 nkhani