15 Anati, Tidzacitanji naye mkazi wamkuru Vasiti monga mwa malamulo, popeza sanacita comuuza mfumu Ahaswero mwa adindo?
Werengani mutu wathunthu Estere 1
Onani Estere 1:15 nkhani