4 pamene anaonetsa zolemera za ufumu wace waulemu, ndi ulemerero wa ukulu wace woposa, masiku ambiri, ndiwo masiku zana limodzi, mphambu makumi asanu ndi atatu.
Werengani mutu wathunthu Estere 1
Onani Estere 1:4 nkhani