Estere 4:5 BL92

5 Pamenepo Estere anaitana Hataki mdindo wina wa mfumu, amene idamuika amtumikire, namuuza amuke kwa Moredekai, kuti adziwe ici nciani ndi cifukwa cace ninji.

Werengani mutu wathunthu Estere 4

Onani Estere 4:5 nkhani