Estere 4:7 BL92

7 Ndipo Moredekai anamfotokozera zonse zidamgwera, ndi mtengo wace wa ndarama adati Hamani adzapereka m'nyumba ya cuma ca mfumu pa Ayuda, kuwaononga.

Werengani mutu wathunthu Estere 4

Onani Estere 4:7 nkhani