Estere 9:24 BL92

24 popeza Hamani mwana wa Hamedata wa ku Agagi, mdani wa Ayuda onse, adapangira Ayuda ciwembu kuwaononga, naombeza Puri, ndiwo ula, kuwatha ndi kuwaononga;

Werengani mutu wathunthu Estere 9

Onani Estere 9:24 nkhani