29 Pamenepo Estere mkazi wamkuru mwana wa Abihaili, ndi Moredekai Myuda, analembera molamulira, kukhazikitsa kalata uyu waciwiri wa Purimu.
Werengani mutu wathunthu Estere 9
Onani Estere 9:29 nkhani