Zekariya 10:1 BL92

1 Pemphani kwa Yehova mvula, m'nyengo ya mvula ya masika, kwa Yehova wolenga mphezi; ndipo adzawapatsa mibvumbi ya mvula, kwayense zophukira kuthengo.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 10

Onani Zekariya 10:1 nkhani