Zekariya 7:13 BL92

13 Ndipo kunacitika, monga Iye anapfuula, koma iwo sanamvera; momwemo iwo adzapfuula, koma Ine sindidzamva, ati Yehova wa makamu;

Werengani mutu wathunthu Zekariya 7

Onani Zekariya 7:13 nkhani