14 Ndipo nthawi zija ambiri adzaukira mfumu ya kumwela, ndi aciwawa mwa anthu a mtundu wako adzadzikuza kukhazikitsa masomphenyawo, koma adzagwa iwo.
Werengani mutu wathunthu Danieli 11
Onani Danieli 11:14 nkhani