Danieli 11:29 BL92

29 Pa nthawi yoikika adzabwera, nadzalowa kumwela; koma sikudzakhala monga nthawi yoyamba ija, kapena yotsirizayi.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:29 nkhani