28 Ndipo adzabwerera ku dziko lace ndi cuma cambiri; ndi mtima wace udzatsutsana ndi cipangano copatulika, nadzacita cifuniro cace, ndi kubwerera ku dziko lace.
Werengani mutu wathunthu Danieli 11
Onani Danieli 11:28 nkhani