31 Ndipo ankhondo adzamuimirira, nadzadetsa malo opatulika ndi linga lace; nadzacotsa nsembe yosalekezayo, nadzaimitsa conyansa copululutsaco.
Werengani mutu wathunthu Danieli 11
Onani Danieli 11:31 nkhani