Danieli 11:32 BL92

32 Ndipo akucitira coipa cipanganoco iye adzawaipsa, ndi kuwasyasyalika; koma anthu akudziwa Mulungu wao adzalimbika mtima, nadzacita mwamphamvu.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:32 nkhani