33 Ndipo aphunzitsi a anthu adzalangiza ambiri, koma adzagwa ndi lupanga, ndi lawi lamoto, ndi undende, ndi kufunkhidwa masiku ambiri.
Werengani mutu wathunthu Danieli 11
Onani Danieli 11:33 nkhani