26 Mfumu inayankha, niti kwa Danieli, amene dzina lace ndiye Belitsazara, Ukhoza kodi kundidziwitsa lotolo ndidalilota, ndi kumasulira kwace?
Werengani mutu wathunthu Danieli 2
Onani Danieli 2:26 nkhani