Danieli 2:27 BL92

27 Nayankha Danieli pamaso pa mfumu, nati, Cinsinsi inacitira liuma mfumu, angakhale anzeru, openduza, alembi, kapena alauli, sakhoza kuciululira mfumu;

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:27 nkhani