Danieli 3:20 BL92

20 Nauza amuna ena amphamvu a m'khamu lace la nkhondo amange Sadrake, Mesake, ndi Abedinego, ndi kuwaponya m'ng'anjo yotentha yamoto.

Werengani mutu wathunthu Danieli 3

Onani Danieli 3:20 nkhani