21 Pamenepo amuna awa anamangidwa ali cibvalire zopfunda zao, maraya ao, ndi nduwira zao, ndi zobvala zao zina; naponyedwa m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto.
Werengani mutu wathunthu Danieli 3
Onani Danieli 3:21 nkhani