20 Mtengo mudauona umene unakula, nukhala wolimba, nufikira kumwamba msinkhu wace, nuonekera pa dziko lonse lapansi,
Werengani mutu wathunthu Danieli 4
Onani Danieli 4:20 nkhani