14 Ndipo mfumu m'mene atamva mau awa anaipidwa kwambiri, naika mtima wace pa Danieli kuti amlanditse, nayesetsa mpaka polowa dzuwa kumlanditsa.
Werengani mutu wathunthu Danieli 6
Onani Danieli 6:14 nkhani