3 Pamenepo Danieli amene anaposa akuluwa ndi akalonga, popeza munali mzimu wopambana mwa iye, ndi mfumu inati imuike woyang'anira ufumu wonse.
Werengani mutu wathunthu Danieli 6
Onani Danieli 6:3 nkhani