Danieli 7:11 BL92

11 Pamenepo ndinapenyera cifukwa ca phokoso la mau akuru idanena nyangayi; ndinapenyera mpaka adacipha ciromboci, ndi kuononga mtembo wace, ndi kuupereka utenthedwe ndi moto.

Werengani mutu wathunthu Danieli 7

Onani Danieli 7:11 nkhani