Danieli 7:12 BL92

12 Ndipo zirombo zotsalazo anazicotsera ulamuliro wao, koma anatalikitsa moyo wao, ukhalenso nyengo ndi nthawi.

Werengani mutu wathunthu Danieli 7

Onani Danieli 7:12 nkhani