Danieli 7:13 BL92

13 Ndinaona m'masomphenya a usiku, taonani, anadza ndi mitambo ya kumwamba wina ngati mwana wa munthu, nafika kwa Nkhalamba ya kale lomwe; ndipo anamyandikizitsa pamaso pace.

Werengani mutu wathunthu Danieli 7

Onani Danieli 7:13 nkhani