14 Cifukwa cace Yehova wakhala maso pa coipaco, ndi kutifikitsira ico; pakuti Yehova Mulungu wathu ali wolungama mu nchito zace zonse azicita; ndipo sitinamvera mau ace.
Werengani mutu wathunthu Danieli 9
Onani Danieli 9:14 nkhani