Danieli 9:15 BL92

15 Ndipo tsopano, Ambuye Mulungu wathu, amene munaturutsa anthu anu m'dziko la Aigupto ndi dzanja lamphamvu, ndi kudzitengera mbiri monga lero lino, tacimwa, tacita coipa.

Werengani mutu wathunthu Danieli 9

Onani Danieli 9:15 nkhani