11 abwere naye Vasiti mkazi wamkuru pamaso pa mfumu ndi korona wacifumu, kuonetsa anthu ndi akuru kukoma kwace; popeza anali wokongola maonekedwe ace.
Werengani mutu wathunthu Estere 1
Onani Estere 1:11 nkhani