Estere 1:12 BL92

12 Koma Vasiti mkazi wamkuruyo anakana kudza pa mau a mfumu adamuuza adindowo; potero mfumu idapsa mtima ndithu, ndi mkwiyo wace unatentha m'kati mwace.

Werengani mutu wathunthu Estere 1

Onani Estere 1:12 nkhani