Estere 10:3 BL92

3 Pakuti Moredekai Myuda anatsatana naye mfumu Ahaswero, nakhala wamkuru mwa Ayuda, nabvomerezeka mwa unyinji wa abale ace wakufunira a mtundu wace zokoma, ndi wakunena za mtendere kwa mbeu yace yonse.

Werengani mutu wathunthu Estere 10

Onani Estere 10:3 nkhani