Yobu 1:1 BL92

1 PANALI munthu m'dziko la Uzi, dzina lace ndiye Yobu; ndipo munthuyu anali wangwiro ndi woongoka, wakuopa Mulungu ndi kupewa zoipa.

Werengani mutu wathunthu Yobu 1

Onani Yobu 1:1 nkhani