Estere 2:23 BL92

23 Ndipo atafunsira mlanduwo, anaupeza momwemo, napacikidwa onse awiri pamtengo; ndipo anacilemba m'buku la mbiri pamaso pa mfumu.

Werengani mutu wathunthu Estere 2

Onani Estere 2:23 nkhani