Estere 3:1 BL92

1 Zitatha izi, mfumu Ahaswero anamkuza Hamani mwana wa Hamedata, wa ku Agagi, namkweza, naika mpando wace upose akalonga onse okhala naye.

Werengani mutu wathunthu Estere 3

Onani Estere 3:1 nkhani