10 Ndipo mfumu inabvula mphete yace pa cala cace, naipereka kwa Hamani mwana wa Hamedata wa ku Agagi, mdani wa Ayuda.
Werengani mutu wathunthu Estere 3
Onani Estere 3:10 nkhani