11 Ndipo mfumu idati kwa Hamani, Siliva akhale wako, ndi anthu omwe; ucite nao monga momwe cikukomera.
Werengani mutu wathunthu Estere 3
Onani Estere 3:11 nkhani