3 Ninena naye mfumu, Mufunanji, Estere mkazi wamkuru? pempho lanu nciani? lidzaperekedwa kwa inu, kufikira limodzi la magawo awiri a ufumuwo.
Werengani mutu wathunthu Estere 5
Onani Estere 5:3 nkhani