Nehemiya 10:32 BL92

32 Tinadziikiranso malamulo, kuti tizipereka caka ndi caka limodzi la magawo atatu a sekeli ku nchito ya nyumba ya Mulungu wathu;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 10

Onani Nehemiya 10:32 nkhani