Nehemiya 11:11 BL92

11 Seraya mwana wa Hilikiya, mwana wa Mesulamu, mwana wa Zadoki, mwana wa Merayoti, mwana wa Ahitubu mtsogoleri wa m'nyumba ya Mulungu;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 11

Onani Nehemiya 11:11 nkhani