13 ndi abale ace akulu a nyumba za makolo awiri mphambu makumi anai kudza awiri, ndi Amasai mwana wa Azareli, mwana wa Azai, mwana wa Mesilimoti, mwana wa Imeri;
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 11
Onani Nehemiya 11:13 nkhani