Nehemiya 11:24 BL92

24 Ndi Petatiya mwana wa Mesezabele, wa ana a Zera, mwana wa Yuda, anatumikira mfumu pa mirandu yonse ya anthuwo.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 11

Onani Nehemiya 11:24 nkhani