Nehemiya 11:30 BL92

30 Zanowa, Adulamu ndi midzi yao, Lakisi ndi minda yace, Azeka ndi miraga yace. Ndipo anamanga misasa kuyambira ku Beereseba mpaka cigwa ca Hinomu.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 11

Onani Nehemiya 11:30 nkhani