23 Ana a Levi, akuru a nyumba za makolo, analembedwa m'buku la macitidwe, mpaka masiku a Yohanana mwana wa Eliasibu.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 12
Onani Nehemiya 12:23 nkhani