37 ndi ku cipata ca kucitsime, ndi kundunji kwao, anakwerera pa makwerero a mudzi wa Davide, potundumuka linga, popitirira pa nyumba ya Davide, mpaka ku cipata ca kumadzi kum'mawa.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 12
Onani Nehemiya 12:37 nkhani