28 Koma wina wa ana a Yoyada, mwana wa Eliasibu mkuru wa ansembe, anali mkamwini wa Sanibalati Mhoroni; cifukwa cace ndinampitikitsa kumcotsa kwa ine.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 13
Onani Nehemiya 13:28 nkhani