Nehemiya 13:30 BL92

30 Momwemo ndinawayeretsa kuwacotsera acilendo onse, ndi kuikira udikiro ansembe ndi Alevi, yense ku nchito yace;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 13

Onani Nehemiya 13:30 nkhani