9 Pamenepo ndinalamulira, ndipo anayeretsa zipindazo; ndipo ndinabwezeramonso zipangizo za nyumba ya Mulungu, pamodzi ndi zopereka za ufa ndi libano.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 13
Onani Nehemiya 13:9 nkhani