14 Ndi cipata ca kudzala anacikonza Malikiya mwana wa Rekabu, mkuru wa dziko la Bete Hakeremu; anacimanga, naika zitseko zace, zokowera zace, ndi mipiringidzo yace.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 3
Onani Nehemiya 3:14 nkhani